Hymn 42 Masiku tikatsala ife treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 42 Masiku tikatsala ife Masiku tikatsala ife M’dziko mwathu momwe Mulungu watipatsa ntchito, Tikazigwiritse. Pamene zakuipa zathu Zisautsa ife, Tikapemphera Mbuye wathu Atipulumutse.