Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 4 Ndinu wakuyera!
Ndinu wakuyera!
Zakumwamba zonse
Ndi zapansi zitamabe
Dzina lanulo
Mlengi wachifundo.
Mphambi, Ambuyathu,
E! Mlungu Mmodzi,
Mwa Atatuwo.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 4 Ndinu wakuyera!
Ndinu wakuyera!
Zakumwamba zonse
Ndi zapansi zitamabe
Dzina lanulo
Mlengi wachifundo.
Mphambi, Ambuyathu,
E! Mlungu Mmodzi,
Mwa Atatuwo.