Hymn 35 Zonse za m’dziko zidzatha, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 35 Zonse za m’dziko zidzatha, Zonse za m’dziko zidzatha, Koma za moyo m’Mwamba Zomwe zidzakhalitsatu, Chakatu ndi chaka.