Hymn 319 Koma zina sizinadziwa ayi, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 319 Koma zina sizinadziwa ayi, Koma zina sizinadziwa ayi, Makwawa ‘napyola ‘ye, ndi mdima woopsa wa usikuwo Ambuye nailonda yake. Anamva kulira kutaliko, Naipeza yofoka, yakufayo.