Hymn 271 Pomwalira Mbuyeyo treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 271 Pomwalira Mbuyeyo Pomwalira Mbuyeyo Anapfuula kokweza Naitana Atate Kupereka mzimu wake; “Mlungu wanga, Mlungu wanga, Mwandisiy’ranjitu Ine, Mundikweze m’Mwambamo, Landirani mzimu wanga.”