Hymn 266 Ukondwere moyo wanga, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 266 Ukondwere moyo wanga, Ukondwere moyo wanga, Kuunika kuoneka, Ndi mdimawo uthawatu; Lulutira moyo wanga.