Hymn 264 Bvinabvina moyo wanga, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 264 Bvinabvina moyo wanga, Bvinabvina moyo wanga, Lulutira mtima wanga; Wa mawuwo a Yehova Watuluka m’dziko lako.