Hymn 262 Tumphatumpha moyo wanga, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 262 Tumphatumpha moyo wanga, Tumphatumpha moyo wanga, Sangalala ndi Mtetezi; Kuwombola kwa Yehova Kwatuluka m’dziko lako.