Hymn 240 Nyama za m’thengo treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 240 Nyama za m’thengo Nyama za m’thengo Ndi mbalamezo Zili nazo zogonamo, Koma Mwana wa Mlungu Analibe nyumba, M’mapululu nagonatu.