Hymn 220 Kalekale ndinathawa, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 220 Kalekale ndinathawa, Kalekale ndinathawa, Ndinakana kumvera Inu; Koma lero ndamva kuti Muli Mwini wake wa moyo.