Hymn 200 Ndi tsopano tilindira treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 200 Ndi tsopano tilindira Ndi tsopano tilindira M’dziko lathu lino; Ntchito atipatsa Mlungu, Tizigwira bwino.