Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 188 Ine ndili ndi manyazi
Ine ndili ndi manyazi
Kuti kale lomwelo
Ndinanyoza kudza komwe
Kwa Mtetezi wanga Yesu,
Ndati sindimfuna ‘yi.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 188 Ine ndili ndi manyazi
Ine ndili ndi manyazi
Kuti kale lomwelo
Ndinanyoza kudza komwe
Kwa Mtetezi wanga Yesu,
Ndati sindimfuna ‘yi.