Hymn 1846 Mtima wanga uyamike treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1846 Mtima wanga uyamike Mtima wanga uyamike Mfumu Yakumwambako; Anandiwombola ine Nanditsuka m’mtimamo.