Hymn 1835 Mtima wanga lemekeza treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1835 Mtima wanga lemekeza Mtima wanga lemekeza Mlungu wako ndi chimwemwe. Nthawi zonse ndimtamanda; Ndimwimbira nyimbo zanga. Moyo, mphamvu, nzeru zonse, Zidzamlemekeza konse.