Hymn 177 Tate, ndili mwana wanu, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 177 Tate, ndili mwana wanu, Tate, ndili mwana wanu, Nkana ndinachimwa, Ndingolirira kwa Inu; Khululukireni.