Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1700 Ambuye Mwini moyo,
Ambuye Mwini moyo,
Kokoma mnafumako;
Ndizizwa pomva mawu
Umo mwachitiramo.
Chisoni chija chanu
Mcha pamachimo anga,
Mwasaukira Inu
Kupalamula kwanga.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1700 Ambuye Mwini moyo,
Ambuye Mwini moyo,
Kokoma mnafumako;
Ndizizwa pomva mawu
Umo mwachitiramo.
Chisoni chija chanu
Mcha pamachimo anga,
Mwasaukira Inu
Kupalamula kwanga.