Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1699 A! Mutu wakuyera,
A! Mutu wakuyera,
Wolaswa wachisoni,
Abveka Inu anthu
Ndi minga ya udani;
Ambuye mwafokatu
Ndi masauko aja,
Mwatuwa m’maso mwanu,
Mumayerera kale.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1699 A! Mutu wakuyera,
A! Mutu wakuyera,
Wolaswa wachisoni,
Abveka Inu anthu
Ndi minga ya udani;
Ambuye mwafokatu
Ndi masauko aja,
Mwatuwa m’maso mwanu,
Mumayerera kale.