Hymn 1697 Onani m’mutu, m’manjanso treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1697 Onani m’mutu, m’manjanso Onani m’mutu, m’manjanso Mudzera nsoni m’mwazimo. A! panalibe kalelo Wondibvalira mingayo.