Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1669 Ukafuna kumdziwitsa,
Ukafuna kumdziwitsa,
Akondadi!
Uzimpatsa moyo wako,
Akondadi!
Kodi umachita mantha?
Pena umadera nkhawa?
Yesu amasangalatsa
Akondadi!
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1669 Ukafuna kumdziwitsa,
Ukafuna kumdziwitsa,
Akondadi!
Uzimpatsa moyo wako,
Akondadi!
Kodi umachita mantha?
Pena umadera nkhawa?
Yesu amasangalatsa
Akondadi!