Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1668 Kumdziwitsa ndiko moyo,
Kumdziwitsa ndiko moyo,
Akondadi!
Akhumbira mtima wako
Akondadi!
Mwazi wake ngwowombola,
M’chipululu wakufuna,
M’khola mwake akusunga,
Akondadi!
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1668 Kumdziwitsa ndiko moyo,
Kumdziwitsa ndiko moyo,
Akondadi!
Akhumbira mtima wako
Akondadi!
Mwazi wake ngwowombola,
M’chipululu wakufuna,
M’khola mwake akusunga,
Akondadi!