Hymn 163 Mukonda nyimbo za ana, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 163 Mukonda nyimbo za ana, Mukonda nyimbo za ana, Kokoma amaimbatu; Ndi ana athu atama Atate, Mwana ndi Mzimu.