Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1612 Adzadza indetu
Adzadza indetu
Kudziko linoli;
Tidzanka nayeyu
M’ufumu wakedi.
Momwemo tidzampenya ‘Ye,
Momwemo tidzakhala ‘fe,
Nkuwala kwake koti mbee!
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1612 Adzadza indetu
Adzadza indetu
Kudziko linoli;
Tidzanka nayeyu
M’ufumu wakedi.
Momwemo tidzampenya ‘Ye,
Momwemo tidzakhala ‘fe,
Nkuwala kwake koti mbee!