Hymn 1608 Yesu, dzina lakukonda treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1608 Yesu, dzina lakukonda Yesu, dzina lakukonda La Mwanayo wa Mulungu, Ife anthu osauka Tithawira nalo kwanu.