Hymn 1607 Yesu, dzina ndi lomweli treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1607 Yesu, dzina ndi lomweli Yesu, dzina ndi lomweli La pa dziko lino lonse, Ndi la mphamvu yolanditsa Anthu mu masoka onse.