Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 156 Yesu Mbuye, onani
Yesu Mbuye, onani
Tadza poitana Inu;
M’dzina lanu tifika
Osekera kwa Atate;
Mkhale nafe Inu nokha
Tikaimba nkupemphera.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 156 Yesu Mbuye, onani
Yesu Mbuye, onani
Tadza poitana Inu;
M’dzina lanu tifika
Osekera kwa Atate;
Mkhale nafe Inu nokha
Tikaimba nkupemphera.