Hymn 148 Ndisauka, ndimasowa treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 148 Ndisauka, ndimasowa Ndisauka, ndimasowa Mphamvu ya kuyera m’mtima, Mwazi wanu wanditsuka; Mwana Mlungu, ndingubwera.