Site icon Treasure Hymns – Chichewa

Hymn 1479 Ndi Yesu yemwe kalelo

Chichewa Believers Christian Hymns

Hymn 1479 Ndi Yesu yemwe kalelo

 

Ndi Yesu yemwe kalelo

‘Nakhala munthu pansipa;

Anthenda onse nthawiyo

Nachira yake mphamvuyo.

Exit mobile version