Hymn 1473 Anasenza pa bwanji uchimo wonsewo, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1473 Anasenza pa bwanji uchimo wonsewo, Anasenza pa bwanji uchimo wonsewo, Ngati wanu pa Yesu sulipo? Bwanji mwazi wakhetsa kutsuka ifetu, Ngati uwu sitikwanako?