Hymn 147 Ndisauka, ndinachimwa, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 147 Ndisauka, ndinachimwa, Ndisauka, ndinachimwa, Koma Inu mnandifera, Ndimo ndamva mund’itana; Mwana Mlungu, ndingubwera.