Hymn 1465 Akulu inu m’bwere nonse, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1465 Akulu inu m’bwere nonse, Akulu inu m’bwere nonse, Ana inu nomwe, Ambuye akuitanani, Bvomerani nonse.