Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1451 Okoma ndiwo mawu
Okoma ndiwo mawu
A Yesu Mbuyeyo,
Wopatsa ife anthu
Mtendere wakowo.
Kwa ife akumvera
Kulibe mantha ‘yi;
Timamva liu lake
Lingoti, Mudza ‘nu.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1451 Okoma ndiwo mawu
Okoma ndiwo mawu
A Yesu Mbuyeyo,
Wopatsa ife anthu
Mtendere wakowo.
Kwa ife akumvera
Kulibe mantha ‘yi;
Timamva liu lake
Lingoti, Mudza ‘nu.