Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1424 Malo anachepa,
Malo anachepa,
Nyumba anammana,
Agona m’modyera,
Mutu paudzuwo.
Anthu sanamtama,
Nyimbo panalibe,
M’nyumba ya alendo
Malo munalibe.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1424 Malo anachepa,
Malo anachepa,
Nyumba anammana,
Agona m’modyera,
Mutu paudzuwo.
Anthu sanamtama,
Nyimbo panalibe,
M’nyumba ya alendo
Malo munalibe.