Hymn 1416 Mbuye wanga ndilikumva, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1416 Mbuye wanga ndilikumva, Mbuye wanga ndilikumva, Ndikondana nanu; Umapuma mzimu wanga; Kwathu ndiko kwanu.