Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1398 Nditama mphamvu yake
Nditama mphamvu yake
Ya Mlungu yondizinga;
N’kafoka an’limbitsa,
N’kadwala andichiza.
Pakundisiya bwenzi
Mulungu ali paja;
N’kalowa imfa ine
Alipo Mlungu wanga.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1398 Nditama mphamvu yake
Nditama mphamvu yake
Ya Mlungu yondizinga;
N’kafoka an’limbitsa,
N’kadwala andichiza.
Pakundisiya bwenzi
Mulungu ali paja;
N’kalowa imfa ine
Alipo Mlungu wanga.