Hymn 1397 Okwawa pansi inu, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1397 Okwawa pansi inu, Okwawa pansi inu, Oyenda m’madzi inu, Oyesa dziko nkwanu, Am’mlengalenga inu, Nonsenu ntchito zake Muona tsiku n’tsiku, Saleka kusamala Ndi kudalitsa inu.