Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1342 Tadza kumtsinjeku
Tadza kumtsinjeku
Wa moyo weni,
Chiza zowawazo
Za m’mtimamo;
Mtsinje wodzalawo,
Wokwaniratuwo
Yesu sakana ‘yi;
Idzatu ‘we.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1342 Tadza kumtsinjeku
Tadza kumtsinjeku
Wa moyo weni,
Chiza zowawazo
Za m’mtimamo;
Mtsinje wodzalawo,
Wokwaniratuwo
Yesu sakana ‘yi;
Idzatu ‘we.