Hymn 1328 Ndani afuna kunkako treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1328 Ndani afuna kunkako Ndani afuna kunkako Kukazipeza nkhosazo? Ndani adzathandizako Kuti zifunde m’kholamo?