Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1312 Wina sindifuna ‘yi,
Wina sindifuna ‘yi,
Zokhutitsa nzanuzo;
M’utsetu akugwawo,
Mchizetu odwalawo.
Ndine wakuipa bii!
Ndinu wakuyera mbuu!
Ndimadzala tchimoli,
Wolungama ndinutu.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1312 Wina sindifuna ‘yi,
Wina sindifuna ‘yi,
Zokhutitsa nzanuzo;
M’utsetu akugwawo,
Mchizetu odwalawo.
Ndine wakuipa bii!
Ndinu wakuyera mbuu!
Ndimadzala tchimoli,
Wolungama ndinutu.