Hymn 1308 Ndi ine, m’mtima Mwanu mbee! treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1308 Ndi ine, m’mtima Mwanu mbee! Ndi ine, m’mtima Mwanu mbee! Mokoma ndingakhalebe, Ndikhale wanu wanudi; Ndagonjatu Mbuyanga ‘Nu.