Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1286 E, ndikukhulupirani,
E, ndikukhulupirani,
Ndauona mwazi wanu;
Tere ndikugwadirani,
Tere ndapachikwa nanu.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1286 E, ndikukhulupirani,
E, ndikukhulupirani,
Ndauona mwazi wanu;
Tere ndikugwadirani,
Tere ndapachikwa nanu.