Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1275 Mtima ‘we siya ndi Yesu nsonizi,
Mtima ‘we siya ndi Yesu nsonizi,
Usabisa tchimo lakoli;
Zichuluka mphamvu zakezi,
Likusunga dzanja lakeli;
Bwera kwa Mbuyathu leroli mwana ‘we,
Bwera kwa Mbuyathu leroli mwana ‘we.
