Hymn 1241 Ati: Mwana, kumbukira treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1241 Ati: Mwana, kumbukira Ati: Mwana, kumbukira Zonse ndinakuchitira; Ndakukonda, ndakuferea, Ndakufuna posokera.