Hymn 1227 Ndiyamika Mbuye wanga treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1227 Ndiyamika Mbuye wanga Ndiyamika Mbuye wanga Ndidzamlemekezabe; Ndipititsa mbiri yake Ya kukonda kwakeko.