Hymn 1223 Ndidzaimba za Mulungu, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1223 Ndidzaimba za Mulungu, Ndidzaimba za Mulungu, Za kukonda kwakeko; Anatuma Mwana wake Kundifera kalelo.