Hymn 1213 Mwamva Yesu m’mtimamo, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1213 Mwamva Yesu m’mtimamo, Mwamva Yesu m’mtimamo, Adzanso kawiri, M’mene ali nanutu Muli ndi chimwemwe. Ntchito zachifundozi Iye watha izi, Kuti mwawo m’Mwambamo Naye tikhalebe.