Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1209 Mnyamata wake ndinetu,
Mnyamata wake ndinetu,
Ndimvera Mawu akewo;
Ndampatsa mtima wonsewu,
Ndimtumikire pansipa.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1209 Mnyamata wake ndinetu,
Mnyamata wake ndinetu,
Ndimvera Mawu akewo;
Ndampatsa mtima wonsewu,
Ndimtumikire pansipa.