Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1198 Mabala ake m’manja
Mabala ake m’manja
Ndaona indetu,
Ndi minga ya pamutu
Yolasa Mbuyeyu;
Etu, wakonda inedi,
Pamtandapo kufera ‘ne.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1198 Mabala ake m’manja
Mabala ake m’manja
Ndaona indetu,
Ndi minga ya pamutu
Yolasa Mbuyeyu;
Etu, wakonda inedi,
Pamtandapo kufera ‘ne.