Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1197 Ndafoka ine kale,
Ndafoka ine kale,
Ndafuna kufaku;
Anadza kundichiza
Zinthenda zangazo;
Ndi mwazi wake woti pyu!
Ndayera nawo m’mtimamu.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1197 Ndafoka ine kale,
Ndafoka ine kale,
Ndafuna kufaku;
Anadza kundichiza
Zinthenda zangazo;
Ndi mwazi wake woti pyu!
Ndayera nawo m’mtimamu.