Hymn 1160 Ndinakhala wakuipa, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1160 Ndinakhala wakuipa, Ndinakhala wakuipa, Ndinamkana kalelo; Koma Yesu waiwala Mphulupulu zangazo.