Hymn 1138 Masiku onse m’mtima mwanga treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1138 Masiku onse m’mtima mwanga Masiku onse m’mtima mwanga Ndili ndi mtenderewo, Chifukwa ndimakhulupira Mtsogoleri wangayo.